Numeri 1:17 - Buku Lopatulika17 Ndipo Mose ndi Aroni anatenga anthu awa, onenedwa maina ao; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Ndipo Mose ndi Aroni anatenga anthu awa, onenedwa maina ao; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Mose ndi Aroni adaŵatenga anthu amene atchulidwaŵa, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Mose ndi Aaroni anatenga anthu amene mayina awo anaperekedwa, Onani mutuwo |