Nehemiya 9:12 - Buku Lopatulika12 Munawatsogoleranso usana ndi mtambo woti njo, ndi moto tolo usiku, kuwaunikira m'njira akayendamo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Munawatsogoleranso usana ndi mtambo woti njo, ndi moto tolo usiku, kuwaunikira m'njira akayendamo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Munkaŵatsogolera masana ndi mtambo, ndipo usiku munkaŵaunikira ndi moto njira imene ankayendamo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Masana munkawunikira ndi chipilala cha mtambo ndipo usiku munkawunikira ndi chipilala cha moto njira yonse imene ankayendamo. Onani mutuwo |