Nehemiya 8:11 - Buku Lopatulika11 Ndipo Alevi anatontholetsa anthu onse, ndi kuti, Khalani muli chete; pakuti lero ndi lopatulika; musamachita chisoni. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndipo Alevi anatontholetsa anthu onse, ndi kuti, Khalani muli chete; pakuti lero ndi lopatulika; musamachita chisoni. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Choncho Alevi adacheteketsa anthu onse naŵauza kuti, “Musalirenso ai, pakuti lero ndi tsiku loyera, choncho musakhale ndi chisoni.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Alevi anakhalitsa bata anthu onse powawuza kuti, “Khalani chete, pakuti lero ndi tsiku lopatulika ndipo musakhale ndi chisoni.” Onani mutuwo |