Nehemiya 7:62 - Buku Lopatulika62 ana a Delaya, ana a Tobiya, ana a Nekoda, mazana asanu ndi limodzi mphambu makumi anai kudza awiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201462 ana a Delaya, ana a Tobiya, ana a Nekoda, mazana asanu ndi limodzi mphambu makumi anai kudza awiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa62 A banja la Delaya, a banja la Tobiya, a banja la Nekoda 642. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero62 Zidzukulu za Delaya, zidzukulu za Tobiya ndi zidzukulu za Nekoda 642. Onani mutuwo |