Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Nehemiya 7:45 - Buku Lopatulika

45 Odikira: ana a Salumu, ana a Atere, ana a Talimoni, ana a Akubu, ana a Hatita, ana a Sobai, zana limodzi mphambu makumi atatu kudza asanu ndi atatu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

45 Odikira: ana a Salumu, ana a Atere, ana a Talimoni, ana a Akubu, ana a Hatita, ana a Sobai, zana limodzi mphambu makumi atatu kudza asanu ndi atatu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

45 Alonda a ku Nyumba ya Mulungu anali aŵa: a banja la Salumu, a banja la Atere, a banja la Talimoni, a banja la Akubu, a banja la Hatita, a banja la Sobai, onse pamodzi 138.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

45 Alonda a ku Nyumba ya Mulungu anali awa: Zidzukulu za Salumu, Ateri, Talimoni, Hatita ndi Sobai 138.

Onani mutuwo Koperani




Nehemiya 7:45
6 Mawu Ofanana  

Nadza iwo, naitana mlonda wa mzinda, namfotokozera; ndi kuti, Tinafika ku misasa ya Aaramu, ndipo taonani, palibe munthu pomwepo, kapena mau a munthu, koma akavalo omanga, ndi abulu omanga, ndi mahema ali chimangire.


Ana a odikira: ana a Salumu, ana a Atere, ana a Talimoni, ana a Akubu, ana a Hatita, ana a Sobai, onse pamodzi ndiwo zana limodzi mphambu makumi atatu kudza asanu ndi anai.


Ndi pambali pake anakonza Salumu mwana wa Halohesi, mkulu wa dera lina la dziko la Yerusalemu, iye ndi ana ake akazi.


Oimbira: ana a Asafu, zana limodzi mphambu makumi anai kudza asanu ndi atatu.


Antchito a m'kachisi: ana a Ziha, ana a Hasufa, ana a Tabaoti,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa