Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Nehemiya 7:46 - Buku Lopatulika

46 Antchito a m'kachisi: ana a Ziha, ana a Hasufa, ana a Tabaoti,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

46 Anetini: ana a Ziha, ana a Hasufa, ana a Tabaoti,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

46 Antchito a ku Nyumba ya Mulungu anali aŵa: a banja la Ziha, a banja la Hasufa, a banja la Tabaoti,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

46 Anthu ogwira ntchito ku Nyumba ya Mulungu anali awa: Zidzukulu za Ziha, zidzukulu za Hasufa, zidzukulu za Tabaoti,

Onani mutuwo Koperani




Nehemiya 7:46
9 Mawu Ofanana  

Okhala m'dziko oyamba tsono, akukhala mwaomwao m'mizinda mwao, ndiwo Israele, ansembe, Alevi, ndi Antchito a m'kachisi.


Antchito a m'kachisi: ana a Ziha, ana a Hasufa, ana a Tabaoti,


amenewa anaumirira abale ao, omveka ao, nalowa m'temberero ndi lumbiro, kuti adzayenda m'chilamulo cha Mulungu anachipereka Mose mtumiki wa Mulungu, ndi kuti adzasunga ndi kuchita zonse atilamulira Yehova Ambuye wathu, ndi maweruzo ake, ndi malemba ake;


Awa tsono ndi akulu a dziko okhala mu Yerusalemu; koma m'midzi ya Yuda yense anakhala pa cholowa chake m'midzi mwao, ndiwo Israele, ansembe, ndi Alevi, ndi antchito a m'kachisi, ndi ana a akapolo a Solomoni.


Koma antchito a m'kachisi okhala mu Ofele anakonza kufikira kumalo a pandunji pa Chipata cha Madzi kum'mawa, ndi nsanja yosomphokayo.


Odikira: ana a Salumu, ana a Atere, ana a Talimoni, ana a Akubu, ana a Hatita, ana a Sobai, zana limodzi mphambu makumi atatu kudza asanu ndi atatu.


ana a Kerosi, ana a Siya, ana a Padoni,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa