Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Nehemiya 7:32 - Buku Lopatulika

32 Amuna a ku Betele ndi Ai, zana limodzi mphambu makumi awiri kudza atatu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

32 Amuna a ku Betele ndi Ai, zana limodzi mphambu makumi awiri kudza atatu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

32 Amuna a ku Betele ndi Ai 123.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

32 Anthu a ku Beteli ndi Ai 123

Onani mutuwo Koperani




Nehemiya 7:32
6 Mawu Ofanana  

Anthu a ku Betele ndi Ai, mazana awiri mphambu makumi awiri kudza atatu.


Ana a Benjamini omwe, kuyambira ku Geba pa Mikimasi, ndi Aya, ndi pa Betele ndi midzi yake,


Amuna a ku Mikimasi, zana limodzi mphambu makumi awiri kudza awiri.


Amuna a ku Nebo winayo, makumi asanu kudza awiri.


Ndipo sanatsale mwamuna mmodzi yense mu Ai kapena mu Betele osatulukira kwa Israele; nasiya mzinda wapululu, napirikitsa Israele.


Ndipo Yoswa anawatuma, namuka iwo kulowa m'molalira, nakhala pakati pa Betele ndi Ai, kumadzulo kwa Ai; koma Yoswa anakhala mwa anthu usiku uja.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa