Nehemiya 5:1 - Buku Lopatulika1 Pamenepo panamveka kulira kwakukulu kwa anthu ndi akazi ao kudandaula pa abale ao Ayuda. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Pamenepo panamveka kulira kwakukulu kwa anthu ndi akazi ao kudandaula pa abale ao Ayuda. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Tsono anthu ena pamodzi ndi akazi ao adayamba kudandaula kwambiri chifukwa cha Ayuda anzao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Tsono anthu ena ndi akazi awo anayamba kudandaula kwambiri chifukwa cha Ayuda anzawo. Onani mutuwo |