Nehemiya 4:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo Tobiya Mwamoni anali naye, nati, Chinkana ichi achimanga, ikakwerako nkhandwe, idzagamula linga lao lamiyala. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo Tobiya Mwamoni anali naye, nati, Chinkana ichi achimanga, ikakwerako nkhandwe, idzagamula linga lao lamiyala. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Tobiya Mwamoni amene anali naye adati, “Inde, chimene akumangacho, ngati nkhandwe ikwerapo, idzagwetseratu khoma la miyala laolo.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Tobiya wa ku Amoni, amene anali naye anati, “Chimene akumangacho ngati nkhandwe itakwerapo, itha kugwetsa khoma lawolo!” Onani mutuwo |