Nehemiya 3:9 - Buku Lopatulika9 Ndi pambali pao anakonza Refaya mwana wa Huri, ndiye mkulu wa dera lina la dziko la Yerusalemu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndi pambali pao anakonza Refaya mwana wa Huri, ndiye mkulu wa dera lina la dziko la Yerusalemu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Pambali pa iwowo Refaya, mwana wa Huri, wolamulira theka la dera la mzinda wa Yerusalemu, adakonza chigawo china. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Refaya mwana wa Huri wolamulira theka la chigawo cha Yerusalemu anakonza chigawo china motsatana nawo. Onani mutuwo |