Nehemiya 3:8 - Buku Lopatulika8 Pambali pake anakonza Uziyele mwana wa Haraya, wa iwo osula golide. Ndi padzanja pake anakonza Hananiya, wa iwo osanganiza zonunkhira; nalimbikitsa Yerusalemu mpaka linga lachitando. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Pambali pake anakonza Uziyele mwana wa Haraya, wa iwo osula golide. Ndi padzanja pake anakonza Hananiya, wa iwo osanganiza zonunkhira; nalimbikitsa Yerusalemu mpaka linga lachitando. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Pambali pa iwowo Uziyele, mwana wa Haraiya, wa m'gulu la amisiri osula golide, adakonza chigawo china. Pambali pa iyeyo Hananiya, mmodzi mwa anthu oyenga mafuta onunkhira, adakonza chigawo china. Onsewo adakonza Yerusalemu mpaka ku Khoma Lotambasuka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Pambali pawo Uzieli mwana wa Harihaya wa mʼgulu amisiri osula golide anakonzanso chigawo china. Pambali pake Hananiya mmodzi mwa anthu oyenga mafuta onunkhira, anakonzanso chigawo china. Iwo anakonzanso Yerusalemu mpaka ku Khoma Lotambasuka. Onani mutuwo |