Nehemiya 2:11 - Buku Lopatulika11 Motero ndinafika ku Yerusalemu, ndi kukhalako masiku atatu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Motero ndinafika ku Yerusalemu, ndi kukhalako masiku atatu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Choncho ndidafika ku Yerusalemu ndipo ndidakhala kumeneko masiku atatu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Ndinafika ku Yerusalemu, ndipo ndinakhala kumeneko masiku atatu. Onani mutuwo |