Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Nehemiya 13:20 - Buku Lopatulika

20 Momwemo eni malonda ndi ogulitsa malonda ali onse, anagona kunja kwa Yerusalemu kamodzi kapena kawiri.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

20 Momwemo eni malonda ndi ogulitsa malonda ali onse, anagona kunja kwa Yerusalemu kamodzi kapena kawiri.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

20 Motero anthu amalonda ogulitsa zinthu zamitundumitundu ankagona kunja kwa mzinda wa Yerusalemu kamodzi kapena kaŵiri konse.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

20 Choncho kamodzi kapena kawiri anthu amalonda ndi anthu ogulitsa katundu osiyanasiyana ankagona usiku wonse kunja kwa Yerusalemu.

Onani mutuwo Koperani




Nehemiya 13:20
2 Mawu Ofanana  

Ndipo kunali, kukadayamba chizirezire pa zipata za Yerusalemu, losafika Sabata, ndinawauza atseke pamakomo; ndinawauzanso kuti asatsegulepo, koma litapita Sabata ndipo; ndipo ndinaimika anyamata anga ena pazipata, kuti pasalowe katundu tsiku la Sabata.


Koma ndinawachitira umboni wakuwatsutsa, ndinanena nao, Mugoneranji pafupi pa linga? Mukateronso ndikuthirani manja. Kuyambira pomwepo sanafikenso pa Sabata.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa