Nehemiya 13:11 - Buku Lopatulika11 Potero ndinatsutsana nao olamulira, ndinati, Yasiyidwiranji nyumba ya Mulungu? Ndipo ndinawasonkhanitsa, ndi kuwaika m'malo mwao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Potero ndinatsutsana nao olamulira, ndinati, Yasiyidwiranji nyumba ya Mulungu? Ndipo ndinawasonkhanitsa, ndi kuwaika m'malo mwao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Choncho ndidaŵadzudzula akuluakulu aja kuti, “Kodi chifukwa chiyani Nyumba ya Mulungu yasiyidwa chonchi?” Ndipo ndidasonkhanitsa anthu aja ndi kuŵaikanso pa ntchito zimene ankazigwira Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Choncho ndinadzudzula akuluakulu aja ndipo ndinawafunsa kuti, “Nʼchifukwa chiyani Nyumba ya Mulungu yasiyidwa?” Ndipo ine ndinawayitanitsa pamodzi ndi kuwayika mʼmalo awo. Onani mutuwo |