Nehemiya 12:7 - Buku Lopatulika7 Salu, Amoki, Hilikiya, Yedaya. Awa ndi akulu a ansembe ndi abale ao m'masiku a Yesuwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Salu, Amoki, Hilikiya, Yedaya. Awa ndi akulu a ansembe ndi abale ao m'masiku a Yesuwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Salu, Amoki, Hilikiya, ndi Yedaya. Ameneŵa anali atsogoleri pakati pa ansembe ndi achibale ao pa nthaŵi ya Yesuwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Salu, Amoki, Hilikiya ndi Yedaya. Awa ndiye anali atsogoleri a ansembe ndi abale awo pa nthawi ya Yesuwa. Onani mutuwo |