Nehemiya 12:32 - Buku Lopatulika32 ndi pambuyo pao anayenda Hosaya, ndi limodzi la magawo awiri a akulu a Yuda, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201432 ndi pambuyo pao anayenda Hosaya, ndi limodzi la magawo awiri a akulu a Yuda, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa32 Pambuyo pao pankadza Hosaya ndi theka la akuluakulu aja, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero32 Pambuyo pawo panali Hosayia, theka la atsogoleri a Yuda aja Onani mutuwo |