Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Nehemiya 11:29 - Buku Lopatulika

29 ndi mu Enirimoni, ndi mu Zora, ndi mu Yaramuti,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

29 ndi m'Enirimoni, ndi m'Zora, ndi m'Yaramuti,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

29 ku Enirimoni, ku Zora, ku Yarimuti,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

29 ku Eni-Rimoni, Zora, Yarimuti,

Onani mutuwo Koperani




Nehemiya 11:29
7 Mawu Ofanana  

ndi mu Zikilagi, ndi mu Mekona ndi midzi yake,


Zanowa, Adulamu ndi midzi yao, Lakisi ndi minda yake, Azeka ndi midzi yake. Ndipo anamanga misasa kuyambira ku Beereseba mpaka chigwa cha Hinomu.


mfumu ya ku Yaramuti, imodzi; mfumu ya ku Lakisi, imodzi;


Yaramuti, ndi Adulamu, Soko, ndi Azeka;


Ndipo malire a cholowa chao anali Zora, ndi Esitaoli, ndi Irisemesi;


Ndipo mzimu wa Yehova unayamba kumfulumiza mtima ku misasa ya Dani pakati pa Zora ndi Esitaoli.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa