Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Nehemiya 11:25 - Buku Lopatulika

25 Ndi ana ena a Yuda anakhala m'midzi ya kuminda yao, mu Kiriyati-Ariba ndi midzi yake, ndi mu Diboni ndi midzi yake, ndi mu Yekabizeele ndi midzi yake,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

25 Ndi ana ena a Yuda anakhala m'midzi ya kuminda yao, m'Kiriyati-Ariba ndi milaga yake, ndi m'Diboni ndi milaga yake, ndi m'Yekabizeele ndi midzi yake,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

25 Anthu ena a fuko la Yuda ankakhala ku Kiriyati-Ariba ndi midzi yake, ku Diboni ndi midzi yake, ku Yekabizeele ndi midzi yake.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

25 Anthu ena a fuko la Yuda ankakhala ku Kiriyati-Ariba ndi midzi yake, ku Diboni ndi midzi yake, ku Yekabizeeli ndi midzi yake,

Onani mutuwo Koperani




Nehemiya 11:25
7 Mawu Ofanana  

Ndipo Sara anafa mu Kiriyati-Ariba (ndiwo Hebroni), m'dziko la Kanani; ndipo Abrahamu anadza ku maliro a Sara, kuti amlire.


ndi mu Yesuwa, ndi mu Molada, ndi Betepeleti,


Hesiboni ndi mizinda yake yonse yokhala pachidikha; Diboni, ndi Bamoti-Baala ndi Bete-Baala-Meoni;


kuyambira pa Aroere, wokhala m'mphepete mwa chigwa cha Arinoni, ndi mzinda uli pakati pa chigwa, ndi chidikha chonse cha Medeba mpaka ku Diboni;


Pamenepo Yoswa anamdalitsa, napatsa Kalebe mwana wa Yefune Hebroni likhale cholowa chake.


Koma kale dzina la Hebroni linali mzinda wa Araba, ndiye munthu wamkulu pakati pa Aanaki. Ndipo dziko linapumula nkhondo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa