Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Nehemiya 11:2 - Buku Lopatulika

2 Ndipo anthu anadalitsa amuna onse akudzinenera mwaufulu kuti adzakhala mu Yerusalemu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Ndipo anthu anadalitsa amuna onse akudzinenera mwaufulu kuti adzakhala m'Yerusalemu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Ndipo anthu adayamika anzao onse amene adadzipereka kuti azikhala ku Yerusalemu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Anthu anayamikira onse amene anadzipereka kuti azikhala mu Yerusalemu.

Onani mutuwo Koperani




Nehemiya 11:2
8 Mawu Ofanana  

Mzindawo tsono ndi wachitando, ndi waukulu; koma anthu anali m'mwemo ngowerengeka, nyumba zomwe sizinamangike.


Dalitso la iye akati atayike linandidzera, ndi mtima wa mkazi wamasiye ndinauimbitsa mokondwera.


ngati ziuno zake sizinandiyamike, ngati sanafunde ubweya wa nkhosa zanga;


Anthu anu adzadzipereka eni ake tsiku la chamuna chanu: M'moyera mokometsetsa, mobadwira matanda kucha, muli nao mame a ubwana wanu.


Mupempherere mtendere wa Yerusalemu; akukonda inu adzaona phindu.


polowa dzuwa mumbwezeretu chikolecho, kuti agone m'chovala chake, ndi kukudalitsani; ndipo kudzakukhalirani chilungamo pamaso pa Yehova Mulungu wanu.


Mtima wanga uvomerezana nao olamulira a mu Israele, amene anadzipereka mwaufulu mwa anthu. Lemekezani Yehova.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa