Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Nehemiya 11:15 - Buku Lopatulika

15 Ndi mwa Alevi: Semaya mwana wa Hasubu, mwana wa Azirikamu, mwana wa Hasabiya, mwana wa Buni;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

15 Ndi mwa Alevi: Semaya mwana wa Hasubu, mwana wa Azirikamu, mwana wa Hasabiya, mwana wa Buni;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

15 Alevi anali aŵa: Semaya, mwana wa Hasubu, mwana wa Azirikamu, mwana wa Hasabiya, mwana wa Buni.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

15 Alevi anali awa: Semaya mwana wa Hasubu, mwana wa Azirikamu, mwana wa Hasabiya, mwana wa Buni.

Onani mutuwo Koperani




Nehemiya 11:15
4 Mawu Ofanana  

Ndi a Alevi: Semaya mwana wa Hasubu, mwana wa Azirikamu, mwana wa Hasabiya, a ana a Merari;


Ndipo Salumu mwana wa Kore, mwana wa Ebiyasafu, mwana wa Kora, ndi abale ake a nyumba ya atate wake; Akora anayang'anira ntchito ya utumiki, osunga zipata za Kachisi monga makolo ao; anakhala m'chigono cha Yehova osunga polowera;


ndi abale ao, ngwazi zamphamvu, zana limodzi mphambu makumi awiri kudza asanu ndi atatu; ndi woyang'anira wao ndiye Zabidiele mwana wa Hagedolimu.


ndi Sabetai, ndi Yozabadi, mwa akulu a Alevi, anayang'anira ntchito za pabwalo za nyumba ya Mulungu;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa