Nehemiya 10:7 - Buku Lopatulika7 Mesulamu, Abiya, Miyamini, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Mesulamu, Abiya, Miyamini, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Mesulamu, Abiya, Miyamini, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Mesulamu, Abiya, Miyamini Onani mutuwo |
Ndipo Ezara mlembi anaima pa chiunda cha mitengo adachimangira msonkhanowo; ndi pambali pake padaima Matitiya, ndi Sema, ndi Anaya, ndi Uriya, ndi Hilikiya, ndi Maaseiya, kudzanja lamanja lake; ndi kudzanja lamanzere Pedaya, ndi Misaele, ndi Malikiya, ndi Hasumu, ndi Hasibadana, Zekariya, ndi Mesulamu.