Nehemiya 10:3 - Buku Lopatulika3 Pasuri, Amariya, Malikiya, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Pasuri, Amariya, Malikiya, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Pasuri, Amariya, Malakiya, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Pasuri, Amariya, Malikiya, Onani mutuwo |
Ndipo Ezara mlembi anaima pa chiunda cha mitengo adachimangira msonkhanowo; ndi pambali pake padaima Matitiya, ndi Sema, ndi Anaya, ndi Uriya, ndi Hilikiya, ndi Maaseiya, kudzanja lamanja lake; ndi kudzanja lamanzere Pedaya, ndi Misaele, ndi Malikiya, ndi Hasumu, ndi Hasibadana, Zekariya, ndi Mesulamu.