Mlaliki 7:1 - Buku Lopatulika1 Mbiri yabwino iposa zonunkhira zabwino; ndi tsiku lakumwalira liposa tsiku lakubadwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Mbiri yabwino iposa zonunkhira zabwino; ndi tsiku lakumwalira liposa tsiku lakubadwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Mbiri yabwino ndi yopambana mafuta onunkhira bwino amtengowapatali. Tsiku lomwalira ndi lopambana tsiku lobadwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Mbiri yabwino ndi yopambana mafuta onunkhira bwino, ndipo tsiku lomwalira ndi lopambana tsiku lobadwa. Onani mutuwo |