Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mlaliki 5:3 - Buku Lopatulika

3 Pakuti loto lafika mwakuchuluka ntchito; ndipo mau a chitsiru mwakuchuluka maneno.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Pakuti loto lafika mwakuchuluka ntchito; ndipo mau a chitsiru mwakuchuluka maneno.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Kuchuluka kwa mavuto mu mtima kumabweretsa maloto oipa, ndipo kuchuluka kwa mau kumadzetsa uchitsiru.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Kuchuluka kwa mavuto mu mtima kumabweretsa maloto oyipa, ndipo kuchuluka kwa mawu kumadzetsa uchitsiru.

Onani mutuwo Koperani




Mlaliki 5:3
5 Mawu Ofanana  

Kodi mau ochulukawa sayenera kuwayankha? Ndi munthu wa milomo ayenera kuyesedwa wolungama?


Pochuluka mau zolakwa sizisoweka; koma wokhala chete achita mwanzeru.


Lilime la anzeru linena bwino zomwe adziwa; koma m'kamwa mwa opusa mutsanulira utsiru.


Nena ndi ana a Israele, nuti nao, Pamene munthu achita chowinda cha padera, anthuwo azikhala a Yehova monga mwa kuyesa kwako.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa