Mika 6:2 - Buku Lopatulika2 Tamverani, mapiri inu, chitsutsano cha Yehova, ndi inu maziko olimba a dziko lapansi; pakuti Yehova ali nacho chitsutsano ndi anthu ake, ndipo adzatsutsana ndi Israele. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Tamverani, mapiri inu, chitsutsano cha Yehova, ndi inu maziko olimba a dziko lapansi; pakuti Yehova ali nacho chitsutsano ndi anthu ake, ndipo adzatsutsana ndi Israele. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Imvani mlandu wa Chauta, inu mapiri, ndi inunso maziko amuyaya a dziko lapansi. Chautatu akuimba mlandu anthu ake, akutsutsana ndi Aisraele. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Imvani mlandu wa Yehova, inu mapiri; tamverani, maziko amuyaya a dziko lapansi. Pakuti Yehova ali ndi mlandu ndi anthu ake; Iye akutsutsa Aisraeli. Onani mutuwo |