Mika 4:5 - Buku Lopatulika5 Pakuti mitundu yonse ya anthu idzayenda, wonse m'dzina la mulungu wake, ndipo ife tidzayenda m'dzina la Yehova Mulungu wathu kunthawi yonka muyaya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Pakuti mitundu yonse ya anthu idzayenda, wonse m'dzina la mulungu wake, ndipo ife tidzayenda m'dzina la Yehova Mulungu wathu kunthawi yonka muyaya. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Mitundu yonse ya anthu imayenda, uliwonse m'njira ya mulungu wake; koma ife tidzayenda m'njira ya Chauta, Mulungu wathu, mpaka muyaya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Mitundu yonse ya anthu itha kutsatira milungu yawo; ife tidzayenda mʼnjira za Yehova Mulungu wathu mpaka muyaya. Onani mutuwo |