Mika 4:4 - Buku Lopatulika4 Koma adzakhala munthu yense patsinde pa mpesa wake, ndi patsinde pa mkuyu wake; ndipo sipadzakhala wakuwaopsa; pakuti pakamwa pa Yehova wa makamu padanena. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Koma adzakhala munthu yense patsinde pa mpesa wake, ndi patsinde pa mkuyu wake; ndipo sipadzakhala wakuwaopsa; pakuti pakamwa pa Yehova wa makamu padanena. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Koma munthu aliyense azidzangodzikhalira mwamtendere patsinde pa mtengo wake wamphesa, ndi patsinde pa mkuyu wake. Palibe amene adzaŵachititsa mantha, pakuti mwiniwake, Chauta Wamphamvuzonse, wanena zimenezi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Munthu aliyense adzakhala pansi pa tsinde pa mtengo wake wa mpesa ndi pa tsinde pa mtengo wake wamkuyu, ndipo palibe amene adzawachititse mantha, pakuti Yehova Wamphamvuzonse wayankhula. Onani mutuwo |