Mika 1:16 - Buku Lopatulika16 Udziyeseze wadazi, udzimete wekha chifukwa cha ana ako okondwera nao; kuza dazi lako ngati la muimba; pakuti anakuchokera, nalowa ndende. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Udziyeseze wadazi, udzimete wekha chifukwa cha ana ako okondwera nao; kuza dazi lako ngati la muimba; pakuti anakuchokera, nalowa ndende. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Inu a ku Yuda, metani mpala, kuwonetsa kuti mukulira ana anu amene munkaŵakonda. Mukhale ndi dazi la dembo poti anawo adakusiyani, adatengedwa ku ukapolo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Metani mipala mitu yanu kuonetsa kuti mukulirira ana anu amene mumawakonda; mudzichititse dazi ngati dembo, pakuti anawo adzatengedwa pakati panu kupita ku ukapolo. Onani mutuwo |