Mateyu 9:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo m'mene anthu a makamu anachiona, anaopa, nalemekeza Mulungu, wakupatsa anthu mphamvu yotere. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo m'mene anthu a makamu anachiona, anaopa, nalemekeza Mulungu, wakupatsa anthu mphamvu yotere. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Anthu onse aja ataona zimenezi, adachita mantha, ndipo adatamanda Mulungu amene adapatsa anthu mphamvu zotere. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Gulu la anthu litaona izi, linadzazidwa ndi mantha ndipo linalemekeza Mulungu amene anapereka ulamuliro kwa anthu. Onani mutuwo |