Mateyu 9:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo ananyamuka, napita kunyumba kwake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo ananyamuka, napita kunyumba kwake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Munthu uja adadzukadi namapita kwao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Ndipo munthuyo anayimirira napita kwawo. Onani mutuwo |