Mateyu 9:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo m'mene Yesu anamva anati, Olimba safuna sing'anga ai, koma odwala. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo m'mene Yesu anamva anati, Olimba safuna sing'anga ai, koma odwala. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Yesu atamva zimenezo, adaŵayankha kuti, “Anthu amene ali bwino sasoŵa sing'anga ai, koma amene akudwala. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Yesu atamva, anati, “Munthu wamoyo safuna singʼanga ayi, koma wodwala. Onani mutuwo |