Mateyu 8:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo m'mene Iye analowa mu Kapernao anadza kwa Iye kenturiyo, nampemba Iye, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo m'mene Iye analowa m'Kapernao anadza kwa Iye kenturiyo, nampemba Iye, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Pamene Yesu ankaloŵa m'mudzi wa Kapernao, mkulu wina wolamulira gulu la asilikali 100 achiroma adadza kwa Iye. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Yesu atalowa mʼKaperenamu, Kenturiyo anabwera kwa Iye napempha chithandizo, Onani mutuwo |