Mateyu 8:31 - Buku Lopatulika31 Ndipo mizimuyo inampempha Iye ninena, Ngati mutitulutsa, mutitumize ife tilowe m'gulu la nkhumbazo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 Ndipo mizimuyo inampempha Iye ninena, Ngati mutitulutsa, mutitumize ife tilowe m'gulu la nkhumbazo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 Tsono mizimu yoipa ija idapempha Yesu kuti, “Mukatitulutsa, bwanji mutitume kuti tikaloŵe m'gulu la nkhumba zili apozo.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 Ndipo ziwandazo zinamupempha Yesu kuti, “Ngati mutitulutsa ife mutitumize mu nkhumba izo.” Onani mutuwo |