Mateyu 8:30 - Buku Lopatulika30 Ndipo panali patali ndi iwo gulu la nkhumba zambiri zilinkudya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 Ndipo panali patali ndi iwo gulu la nkhumba zambiri zilinkudya. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 Pafupi pomwepo pankadya gulu lalikulu la nkhumba. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 Ndipo patali pake panali gulu la nkhumba zimene zimadya. Onani mutuwo |