Mateyu 8:23 - Buku Lopatulika23 Ndipo pamene Iye atalowa m'ngalawa, ophunzira ake anamtsata Iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Ndipo pamene Iye atalowa m'ngalawa, ophunzira ake anamtsata Iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Yesu adaloŵa m'chombo, ndipo ophunzira ake adatsagana naye. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Iye atalowa mʼbwato, ophunzira ake anamutsatira. Onani mutuwo |