Mateyu 8:21 - Buku Lopatulika21 Ndipo wina wa ophunzira ake anati kwa Iye, Ambuye, mundilole ine ndiyambe ndamuka kuika maliro a atate wanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Ndipo wina wa ophunzira ake anati kwa Iye, Ambuye, mundilole ine nditange ndamuka kuika maliro a atate wanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Wophunzira wake wina adauza Yesu kuti, “Ambuye, mundilole ndiyambe ndakaika maliro a atate anga.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Wophunzira wina anati kwa Iye, “Ambuye, mundilole ndiyambe ndakayika maliro a abambo anga.” Onani mutuwo |