Mateyu 7:23 - Buku Lopatulika23 Ndipo pamenepo ndidzafukulira iwo, Sindinakudziweni inu nthawi zonse; chokani kwa Ine, inu akuchita kusaweruzika. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Ndipo pamenepo ndidzafukulira iwo, Sindinakudziwani inu nthawi zonse; chokani kwa Ine, inu akuchita kusaweruzika. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Apo Ine ndidzaŵauza poyera kuti, ‘Sindidaakudziŵani konse. Chokani apa, anthu ochita zoipa.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Pamenepo ndidzawawuza momveka bwino kuti, ‘Sindinakudziweni inu. Chokani kwa Ine, inu ochita zoyipa!’ Onani mutuwo |