Mateyu 7:16 - Buku Lopatulika16 Mudzawazindikira ndi zipatso zao. Kodi atchera mphesa paminga, kapena nkhuyu pamtula? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Mudzawazindikira ndi zipatso zao. Kodi atchera mphesa paminga, kapena nkhuyu pamtula? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Mudzaŵadziŵira zochita zao. Kodi mitengo yaminga nkubala mphesa? Kodi mitula nkubala nkhuyu? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Mudzawazindikira iwo ndi zipatso zawo. Kodi anthu amathyola mpesa pa mtengo wa minga, kapena nkhuyu pa nthula? Onani mutuwo |