Mateyu 6:29 - Buku Lopatulika29 koma ndinena kwa inu, kuti angakhale Solomoni mu ulemerero wake wonse sanavale monga limodzi la amenewa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 koma ndinena kwa inu, kuti angakhale Solomoni mu ulemerero wake wonse sanavale monga limodzi la amenewa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 Komatu kunena zoona, ngakhale mfumu Solomoni yemwe, mu ulemerero wake wonse, sankavala zokongola kulingana ndi limodzi lomwe mwa maluŵa ameneŵa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 Ndikukuwuzani kuti angakhale Solomoni mu ulemerero wake sanavale mofanana ndi limodzi la maluwa amenewa. Onani mutuwo |