Mateyu 6:22 - Buku Lopatulika22 Diso ndilo nyali ya thupi; chifukwa chake ngati diso lako lili la kumodzi, thupi lako lonse lidzakhala lowalitsidwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Diso ndilo nyali ya thupi; chifukwa chake ngati diso lako lili la kumodzi, thupi lako lonse lidzakhala lowalitsidwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 “Maso ndiwo nyale zounikira thupi la munthu. Ngati maso ako ali bwino, m'thupi mwako monse mumakhala kuŵala. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 “Diso ndi nyale ya thupi. Ngati maso ako ali bwino, thupi lako lonse lidzakhala mʼkuwala. Onani mutuwo |