Mateyu 5:33 - Buku Lopatulika33 Ndiponso, munamva kuti kunanenedwa kwa iwo akale, Usalumbire konama, koma udzapereka kwa Ambuye zolumbira zako: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201433 Ndiponso, munamva kuti kunanenedwa kwa iwo akale, Usalumbire konama, koma udzapereka kwa Ambuye zolumbira zako: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa33 “Mudamvanso kuti anthu akale aja adaaŵalamula kuti, ‘Usalumbire monama, koma uchitedi zimene udaŵalonjeza Ambuye molumbira.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero33 “Munamvanso kuti kunanenedwa kwa anthu akale kuti, ‘Musaphwanye lonjezo; koma sungani malonjezo anu amene mwachita kwa Yehova.’ Onani mutuwo |