Mateyu 5:31 - Buku Lopatulika31 Kunanenedwanso, Yense wakuchotsa mkazi wake ampatse iye kalata yachilekaniro: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 Kunanenedwanso, Yense wakuchotsa mkazi wake ampatse iye chilekaniro: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 “Anthu akale aja adaaŵalamulanso kuti, ‘Ngati munthu asudzula mkazi wake, ampatse mkaziyo kalata yachisudzulo.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 “Ananena kuti, ‘Aliyense wosudzula mkazi wake ayenera amupatse kalata ya chisudzulo.’ Onani mutuwo |