Mateyu 5:26 - Buku Lopatulika26 Indetu ndinena ndi iwe, sudzatulukamo konse, koma utalipa kakobiri kakumaliza ndiko. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Indetu ndinena ndi iwe, sudzatulukamo konse, koma utalipa kakobiri kakumaliza ndiko. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Ndithu ndikunenetsa kuti sudzatulukamo mpaka utalipira zonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Zoonadi, Ine ndikukuwuza kuti sudzatuluka mʼndende mpaka utalipira zonse. Onani mutuwo |