Mateyu 4:19 - Buku Lopatulika19 Ndipo Iye ananena nao, Tiyeni pambuyo panga, ndidzakusandutsani asodzi a anthu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ndipo Iye ananena nao, Tiyeni pambuyo panga, ndidzakusandutsani asodzi a anthu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Yesu adaŵauza kuti, “Inu, munditsate, ndikakusandutseni asodzi a anthu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Yesu anati, “Bwerani, tsateni Ine ndipo ndidzakusandutsani asodzi a anthu.” Onani mutuwo |