Mateyu 4:11 - Buku Lopatulika11 Pomwepo mdierekezi anamsiya Iye, ndipo onani, angelo anadza, namtumikira Iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Pomwepo mdierekezi anamsiya Iye, ndipo onani, angelo anadza, namtumikira Iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Pamenepo Satana adamsiya, angelo nkubwera kumadzamutumikira Yesuyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Pamenepo mdierekezi anamusiya ndipo angelo anamutumikira Iye. Onani mutuwo |