Mateyu 3:5 - Buku Lopatulika5 Pamenepo panamtulukira iye a ku Yerusalemu, ndi Yudeya yense, ndi dziko lonse loyandikana ndi Yordani; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Pamenepo panamtulukira iye a ku Yerusalemu, ndi Yudeya lonse, ndi dziko lonse loyandikana ndi Yordani; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Anthu ochokera ku Yerusalemu ndi ku dera lonse la Yudeya, ndi ku madera onse a pafupi ndi mtsinje wa Yordani ankadza kwa iye. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Anthu ankapita kwa iye kuchokera ku Yerusalemu ndi ku Yudeya konse ndi ku madera onse a Yorodani. Onani mutuwo |