Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mateyu 3:13 - Buku Lopatulika

13 Pamenepo Yesu anachokera ku Galileya nadza ku Yordani kwa Yohane, kudzabatizidwa ndi iye.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

13 Pamenepo Yesu anachokera ku Galileya nadza ku Yordani kwa Yohane, kudzabatizidwa ndi iye.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

13 Pa masiku amenewo Yesu adachoka ku Galileya kubwera kwa Yohane ku mtsinje wa Yordani, kuti Yohaneyo amubatize.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

13 Pamenepo Yesu anabwera kuchokera ku Galileya kudzabatizidwa ndi Yohane mu mtsinje wa Yorodani.

Onani mutuwo Koperani




Mateyu 3:13
7 Mawu Ofanana  

Koma pakumva iye kuti Arkelao anali mfumu ya Yudeya m'malo mwa atate wake Herode, anachita mantha kupita kumeneko; ndipo pamene anachenjezedwa ndi Mulungu m'kulota, anamuka nalowa kudziko la Galileya,


Koma Yohane anati amkanize, nanena, Ndiyenera ine kubatizidwa ndi Inu, ndipo Inu mudza kwa ine kodi?


nabatizidwa ndi iye mu mtsinjewo wa Yordani, alikuwulula machimo ao.


Ndipo sindinamdziwe Iye; koma kuti aonetsedwe kwa Israele, chifukwa cha ichi ndinadza ine kudzabatiza ndi madzi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa