Mateyu 28:3 - Buku Lopatulika3 Kuonekera kwake kunali ngati mphezi, ndi chovala chake choyeretsa ngati matalala; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Kuonekera kwake kunali ngati mphezi, ndi chovala chake choyeretsa ngati matalala; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Maonekedwe ake anali ngati a mphezi, ndipo chovala chake chinali choyera chambee. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Maonekedwe ake anali ngati mphenzi ndipo zovala zake zinali mbuu ngati matalala. Onani mutuwo |