Mateyu 28:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo popita tsiku la Sabata, mbandakucha, tsiku lakuyamba la sabata, anadza Maria wa Magadala, ndi Maria winayo, kudzaona manda. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo popita tsiku la Sabata, mbandakucha, tsiku lakuyamba la sabata, anadza Maria wa Magadala, ndi Maria winayo, kudzaona manda. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Tsiku la Sabata ya Ayuda litapita, Maria wa ku Magadala ndi Maria wina uja adabwera mbandakucha pa tsiku lotsatira Sabatalo, kudzaona manda aja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Litapita tsiku la Sabata, mmawa wa tsiku loyamba la Sabata, Mariya wa ku Magadala ndi Mariya wina anapita kukaona manda. Onani mutuwo |