Mateyu 27:53 - Buku Lopatulika53 ndipo anatuluka m'manda mwao pambuyo pa kuuka kwake, nalowa m'mzinda woyera, naonekera kwa anthu ambiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201453 ndipo anatuluka m'manda mwao pambuyo pa kuuka kwake, nalowa m'mzinda woyera, naonekera kwa anthu ambiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa53 Adatuluka m'manda, ndipo Yesu atauka kwa akufa, iwo adaloŵa mu Yerusalemu, Mzinda Wopatulika, anthu ambiri nkumaŵaona. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero53 Anatuluka mʼmanda mwawo, ndipo chitachitika chiukitso cha Yesu, anapita mu mzinda woyera naonekera kwa anthu ambiri. Onani mutuwo |